kumasulira CHISOMO
15/7/2009
Chipangano chatsopano limamasulira chisomo ndi chopereka mosaumira “osati” Mulungu kusintha maonekedwa ndi zochitika pamene amasintha mapangano ndipo kuti anasiya uchimo ndikumati chimenecho ndi chisomo mu chipangano chimene chinasinthidwa ndi kutha. Mu chipangano cha tsopano ndiye kuti IYE AKHALA MWA IFE, kutiphunzitsa ndi kutilimbikitsa potipatsa mphanvu monga chifaniziro chake. “munthawi ino” “Ndinali ndi inu” ndidzakhala ndi inu” kupangitsa kuti musunge malamulo anga ndi kuwachita” kulipira kwa dipo limeli ndikosati Mulungu anasintha maganizo achiyero kapena ungwiro wake umene uli ovomerezeka, koma kuti ANAPEREKA mzimu wake monga chopereka, kwa onse kuyambira kwa ang’ono mpaka kwa a akulu mu chipangano chatsopano, monga mumabuku a Jakobo ndi Yohane yoyamba mumachaputala 1-3 ndimmne amanenera nyengo iyi ya chisomo” Ngati mukudziwa bwino kuti chisomo ndichopereka chosaumira—osati kuti Mulungu kusintha makhalidwe ake ndiye kuti Baibulo lonse lidzanveka bwino ndipo Akolinto yoyamba chputala cha 5 ndi malembo ena sadzachotsedwa mu Baibulo monga momwe Thomas Jefferson (anachitira ndiponso wa Evangelicals anachitira munthawi ino) Zidzamveka bwino kwa ife tonse ndi m’mene Baibulo linaperekedwera. Chopereka chozizwitsa monga m’mene zikunvekeramu.