Zimathandauza Chiani Kukhala Wa Nsembe
Kuchita Zinthu mu njira ya Yesu, (Mzuzu)
Mu bukhu la chibvumbulutso limati Yesu anatigula ife kukhala ufumu wa nsembe kutumikira Mulungu wathu (Chibvumbulutso 5) ngati tonse tingakhale ansembe tiyenera kudziwa kuti kukhala wansembe ndi chiani ngati tikufuna kukhala ndi mphamvu m’moyo mwathu tiyenera kukhala ndi maganizo a Mulungu pamoyo yathu. Yesu anati “pitani ndipo ndidzakhala nanu” Anatiphunzitsa, chitani chifuniro changa ndipo ndidzakupatsani inu moyo ndi mphamvu.
29/8/1996
Download Entire MP3 Album | File size: 25.60MB
- Popanda maudindo – ndife tonse Asembe.
- Kutumukira anthu ndi kuthandiza wina ndi mnzake kukhala Yesu!
- Kuthetsa Mabvuto
- Chida chodabwitsa
- Nyimbo (1)
- Bwelani Mudzapeleke
- Musakwirire Luntha lanu
- Afunseni kuti akhale Ansembe (gawo lo yamba)
- Nyimbo (2)
- Afunseni kuti akhale Ansembe (gawo lo chiwiri)
- Pamene Yesu ali——————chimo silingakhale
- Nyimbo (3)