Kubowoleza Kwa Ulemerero

2003

October 3, 1999, Salima, Africa.

Ngati tikumanga chomanga mwani nyumba uzakhumbila katundu; chochekela nyundo, misomali chomangila, chonenetsa mu nyumba ya Mulungu. Pamakhala katundu wina wofunikila. Ngakhale zili choncho mpingo onenetsa wa Yesu siukhuzidwa mu misonkhano, nthawi zina misonkhano ndi yofunika monga zina zogwilira ntchito, ngati timayimba pamodzi mwa Yesu, pamakhala zinthu zina zimene timaphunzira kuchokera kwa abale ndi alongo. Ngati unapitako ku bwalo la milandu ndi kulakhulapo ndi iwo ngati amawona nthawi ya pa mkono, ndi kupitsa mu thumba mwina kulankhula ndi ena. Oweruza safuna choncho ngati ukuyankhula ndi iyeyo utha kugona kusinza kapenanso kungozisiya choncho kapena kusayankhulapo kanthu, akhoza kunena kwa inu. “tulukani mupite mukachite zenizeni. Mukakonzeka kumvera ineyo, mutha kubweranso. Muntha kuchoka pokhapokha mutazikonzekelatsatso.

Mulungu chimodzimodzi. Tikamayimbira Yesu, ngati timuyimbira mu choonadi Yesu, mitima yathu yimalumikizana naye. Maonekedwe a nkhope yanu, kapenyedwe ka maso anu, mphamvu ya liu lanu kuthekera kwa kukhalabe mumaonekedwe izi ndi zinthu zonse zimene zili mbali ya chiyanjano ndi mfumu ya mafumu. Msonkhano umakhala waphindu, ndipo tsopano ndikupatsani chida misonkhano yimakhala ndi gawo lochepa kusiya ndi moyo wathu mwa Yesu. Momwe tingathandizire abale ndi alongo monga a nsembe. Ngati pali munthu wina wayima pafupi ndi inu pamene mukuyimba pamodzi iye ndi kutaya chidwi mukuyimba, ndi chizindikile kuti akufuna kuthandizidwa. Kuti bvuto lake ndi chiyani. Mumayimbidwe osangalatsa. Kuyimba ndi kulumikizana—kuyimbila mfumu ya ulemelero.

Kwa nthawi zimalankhulidwa mu nyimbo yina, za mubuku na nyimbo za uzimu ngati ndimalankhula ndi Yoswa ndi kusiya mwina kupenya mu mwamba kuona kusagwilizana ndi iye. Ndi pamene pakhala chida chothandiza kumanga nyumba ya Mulungu. Momwe Paulo anenera, “mukangano wa aliyense kuzionetsera kukwanilitsa, mwina kuziyeretsa mwa khristu. Wansembe mwina ansembeyo ayenera kukanganira kuwoneka kwa aliyense moyera mwina kukwanilitsa mwa Khristu. Iyi ndi ntchito yanu mu nyumba ya Mulungu. Osati kukhala ndi kumvela, osati kuyimba kokha, koma baibolo likuti “tiyanganire kwa kuzionetsera mwa aliyense kulungama mwa Khristu”

Ngati wina mwa inuyo ali ndi uchimo mwa mtima wosakhulupira.nde pali zida kukuthandizani kuchita ichi. Ngati muli pamozi ndi aliyense kuimba, mutha kuwona nkhope zina, kuyera? Mutha kugwira chokhacho muona kumbuyo kwa mutu wawo. Koma tsopano tili banja ndipo tingaonane wina ndi mzake ngati ndili kuimba nyimbo kwa inu ndingathe kuona kwa inu ndi kumwetulira ndi kuimba nyimbo ngati monga ndilankhula ndi inu. Ngati ndili ndi mtima wanga ndi kuyimba ngati kuti ndili kulankhula ndi wina wake amene ndili ine. Ngati ndili kuyimba koma osakhudzidwa ndikugwedeza mutu wanga osalabadira ndi kumangoyang’ana uku ndi uko—ndiye uyenera kufunsa iwe kuti zili bwanji ine ndi ubale wanga ndi Yesu. Chodziwika ndi choti pali mabvuto amene ali ndi mgwilizano wanga ndi Yesu ngati ndili kulingalira zina pamene ndili kulankhula ndi iye.

Baibulo limati aKristu wowona monga omwa mkaka, amafuna mkaka wa uzimu wa mau a Mulungu Akristo wowona amafuna chiyanjano ndi Yesu monga mmene makanda afunira mkaka. Yesu anati kuti amene ali ake chilakolako cha nyumba ta Atate chimatidya monga moto kunyeketsa chitsulo. Tili ndi moto mu mafupa amane sangazimitsidwe. Ndipo ngati muona wina amene ali chitsulo chonyowa ndipo moto sikunyeketsa, monga utsi, ndiye pafupi ka kuwathandiza iwowo.

Chimodzi cha zida zothandizira kumanga nyumba ya Mulungu zimene zingakupatseni ngati chida chabwino ndi kukweza miyoyo yathu kwa Mulungu. Ngati mungaone anthu amene Sali okhudzidwa kapena kuzichotsera kapena osasamalira kapena kukhala ongosangalala ndi za Yesu. Ganizani za izi ndipo pemphelani za iwo. Mwina pitani ku nyumba zawo tsiku lililonse. Afunseni mmene ali kumvera, ndipo amene ali kumvera zinthuzo. Nenani “ndaona kuti muli kulalikira naye Yesu ndipo simulinso kuonetsera chikondi kwa iye. Simunali kuika mtima wanu kwa zinthu izi. ndipo ndili odabwa ngati muli ndi mkwiyo pa zinthu zina. Ndi chiti chimene chilli chopambana pa moyo wanu koposa Yesu? Kodi mwalankhura mu nthawi yabwino ndi Yesu mukupemphera kwanu kwapadera? Kapena muli kupezeka chabe mu msonkhano pamene chiyangano ndi iye. Sichili bwino? Choncho ichi ndi njira imodzi imene mungathandizilane nonse pamodzi kukhala mwa Yesu ndikukhala tcheru ndi anthu nonse pamodzi pa malo amodzi. Iyi ndi nira imodzi imene ife ansembe osati ongoonera chabe.

Zimene anthu oipa amanena

Panali munthu oipa tsiku lina otchedwa Kaini mukumbuka Kaini, mwana wa Adamu. Anali oip china chimene ananena ndi choti. Sali osamalira mbale wake. Anthu oipa matero ndithu ife ndife osunga mbale wathu. Timakondana wina ndi mzake kuchokera mu mtima wakuya.

Timalimbana kudzipeleka wina ndi nzake molungama kapena watunthu mwa Yesu. Tidali mu zowawa mkubadwa kwithu mpaka Yesu wakhalamo mwa abale ndi alongo. Izi ndi zimene tinena kwa inu. Nchifukwa chake tabwera kuchokera ma dela onse osiyana a dziko kudzakuwuzani zinthu izi;

Tabwera kudzayetsetsa kudzalengeza kwa inu za chilungamo mwa Yesu. Ndipo muyenera kuchita ichi kwa wina ndi nzake mchilungamo mwa Yesu. Si inu ndi chiyanjano chanu ndi Mulungu. Ndife ambiri koma ndife amodzi mwa Yesu, bukhu loyera likutero. Ngati chala chanu chikudwala kapena chilli ndi vuto lina lake, mumayamba kumva mutu kupweteka, mumamva kuzizira—thupi lanu lonse limaphwanya. Ndizowonanso ndi thupi la Yesu, ngati mmodzi wa ife wavulala mu uzimu tonse timakhudzidwa mu uzimu.

Ndife anthu osunga abale, ngati muwona wina wake amene ali ndi vuto ndi chiyanjano chake ndi Mulungu mkupembedza kapena mukaleledwe ka ana kapena munjila ina, tiyenela kuthandizana wina ndi nzake. Ife mmene tili ambiri ndife amodzi. Ndife amodzi wina ndi mzake kupyola mtunda, kupyolanso zaka. Ndife amodzi ndipo timafanana wina ndi nzake. Ndipo timakondana pothandizana wina ndi mzake kukula mu uzimu.

Ndiye chida mmanja mawanu pakumanga kachisi wa Mulungu ndi kumvetetsana wina ndi mzake—tikakhala malo amodzi. Ndipo ngati muwona wina wake safuna kulowa mwa Mulungu ndi mwa anthu ena.

(ali pano potha chabe nthawi) ndipo ndiowonangedwa, ndiye muyenda kulowa mmiyoyo mwawo ndi mmakomo mwawa ndikuwatenga iwo ndi dzanja ndi kuwathandiza kumukonda Yesu kwambiri. Ndinu woyanganila mbale wanu. Tiyenela kuthandizana wina ndi mnzake. Timvetetsane wina ndi mzake.

Pamene tinayimba nyimbo yotsiliza kodi mudalumikizana ndi mtima wa Mulungu? Ndipo kodi mudayamba mwayangana malo okuzungulilani ngati alipo akuvutika? Ena amene alibe chidwa? Ena amane awukira Mulungu ndipo akufuna machilitso enei eni?

Ena amene ndi ofowoka ndiye sakumvetsetsa bwino, zilipo zina pang’ono mwa zinthu zimenezi. Chifukwa takhala womangidwa ntahwi yayitali, sitinathe kupeleka chidwi ku zinthu izi. ino ndi nthawi imene tiyenela kukula ndi kutengapo gawo mu nyumba ya Mulungu. Tsopano zili m’mznja mwathu pamodzi kutumikila zolinga za Mulungu mu mbadwo wathu. Amen?

Pamene zili zowona kuti zinthu izi zingathe kudzetsa kugawikana, zitha kuwonetsa poyela za mkati mwathu zobisika pamene tinkavina ndi kulambila. Anthu ena amakonda kuwala ndipo ena amadana ndi kuwala. Tsono kukhala koteleku kudzetsa kugawinikana chifukwa ena amakukonda kuwala ndipo ena amadana ndi kuwala. Yesuanati sindinadze kubweretsa Mtendere koma lupanga. Nthawi zina zitha kugawanitsa anthu ambanja wina ndi mzake.

Uthenga Wabwino

Ife tomwe tili ndi mipatuko. Muyenda munjila kumene mwalowela, muwona mtundu yonse ya kugawikana. Mpingo wa Yesu, Nazarene, Lutheran, katolika. Pali kugawinikana kwakukulu. Koma, pano pali uthenga wabwino. Ngati mukhala ngati ufumu wa Mulungu monga chipembedzo chimodzi, ngati mulalika za Yesu lalikani osati chipembedzo, ngati mufuma muthandiza anthu ena—kukonda Yesu kuti tichotse chimo, ndi kukhala abwenzi a Babasiti. Alutherani ndi ena otere, aliyense adzayamba kusiya zizindikiro, ndi zimene zidzachitika muno mu Salima? Pamene aliyense adzabwera ndi kudziwa mabvumbulutso ndi kumamvera iwo uku ndi uko mu misewu. Sipadzakhalanso kusiyana. Koma kusiyana kudzakhala pakati pa ofuna kukonda Yesu ndi amene safuna kukonda Yesu ndi kumvera Yesu. Mmalo mwa zopusa zimene zili zimene tili nazo tsopano kusiyana kudzakhala mu kukondana ndi kumvera ndi osati miyambo yathu, ndipo Yesu adzakhala ndi umboni mu mzinda uno mu umodzi umene sunalipo ndi kale lomwe. Ndi chifukwa chake ndi chofunika kuti mumange mu njira imene tili kulankhura kwa inu lero fikirani miyoyo wanu kwa okhulupilira mu mzinda uno ndi kuthandiza kumanga mu njira imeneyi. Potere sipadzakhalanso kusiyana ndi mayina kusiyana kwa amene akufuna kukonda ndi kumvera Yesu ndi amene angofuna kusewera ndi “chipembedzo” siuthenga wabwino kodi?

Ngati tingaphunzire kukhala motere, miyoyo wa anthu idzasintha. Anthu adzaoneka monga Yesu. Padzakhala wina amene muli kumusamalira kwambiri ndi inu ndi ena onse pamodzi mudzalimbika kuti mumuonetsere watunthu kwa Kristo. Mudzamuona munthu ameneyu kupanga chiganizo chomvera Yesu ndikuona kusinthika mu moyo wa munthuyo. Kodi mukudziwa kuti mudzakwanitsa ngati muli nonse pamodzi ndi abale ndi alongo? Mudzaimba mokweza chifukwa mudzakhala mukuyamika Mulungu pazimene ali kuchita. Simudzaganizo inde, ndiyimbe mokweza ine ndine wa “Pentekositi” mudzayamba kuganiza kuti Yesu wapanga zinthu zopambana moyo wanu. “ndifuna kumuyamika iye.” Zimene tikulankhula lero lino pano—zimene miyoyo wa anthu idzasintha, mmene Yesu adzabwera kwa anthu ake. Ndizimene tidzaimbira nyimbo! Ndizimene tizayamika nazo Mulungu koposa!

Satana adzaonongedwa mu miyoyo yathu ndi zimene tidzayamike nazo Mulungu koposa!

Ndikukuuzani kuti pamene tinayamba kuyenda mu zinthu izi zaka khumi ndi zisanu zapitazo zinali zomvetsa mantha ndi zolimbikitsa kodi muli ndi mantha otere?

Mukuoneka olimbika koposa mmene ine ndinalili chifukwa zinali zobvuta kwa ine poyamba. Koma patapita zaka khumi ndi zisanu ndi zikwi za anthu mu dziko lonse lapansi amene anayamba kuyenda mi zinthu zimenezi ndi zabwino ndipo mantha anatha,choncho Mulungu adzatsinjiliza mu nzeru ndi chikondi pamene mupita patsogolo mu zinthu izi. adzatipatsa zosowa zathu monga mwa kuchulukwa mu ulemerero wake. Zizakhala bwino, adzakhala Atate kwa ife. Adzakhala mphunzitsi ndi otikonda miyoyo yathu. Ndipo tidzapitilira mu njira zobvuta zambiri. Yesu adzapambana mu msewu ndi mzinda yonse uno, adzapambana mu mitima yathu. Pamene mantha, kuzikonda, ndi kunyada zimakhala. Adzatichapa ife ndikumanga ife odzadza ndi afulu mu njira pa zimene sitingafunse kapena kuganizira. Zinthu izi ndi zoona ndipo mudzakhala mu zimenezi ngati mudzatsegule moyo wanu ndi kupita patsogolo.

Pamene Yoshua anapita mu dziko lalonjezo Mulungu anati “osachite mantha” ndipo pamene ansembe anayamba kulowa mu mtsinje kunali kobvuta kwa iwo pang’ono, Baibulo limati sanayendepo njira imeneyi mbuyomu ndipo Mulungu anati “chabwino” ndidzakhala nawe” ndipo zinthu izi ndi zoona kwa inunso. Osati pa malo pano pokha ndi malo ozungulirz mzinda uno. Mulungu adzakhala ndi inu pamane mudzapita patsogolo ndi mau ake. Khalani ndi mphamvu ndi kulimbika! Mulungu akuti “monga ndinali ndi Mose monganso ndinakhala ndi iwe mu nthawi yapitayi choncho ndidzakhala ndi iwenso monga mmene uli kupitira chitsogolo osaopa ai”

Abale ena atalankhulanso popeleka miyoyo yawo.

Abale ndi alongo mwaona zimene zikuchitika pano lero? Tayamba kuona ufumu wa Ansembe. Pamene bvumbulutso libwera kwa wina okhalapo. Woyambayo akhale pansi. Ndipo pamene bvumbulutso lafika kwa winanso ndi winanso!! (kunali kukuwa pokweza mau)

jesuslifetogether.com
chiCheŵa Languages icon
 Share icon