YESU-KRISTO WOWONA … WOSATI ONAMA ZOONA… OSATI OYELEKEZA, MUTU … OSATI ZOPEKA.
Kuitana kwa Mulungu ku dziko lapansi ndiyo malo pamodzi ndi Atate, Mwana ndi Mzimu Woyera—kukhala mkwatibwi wokonzeka kubwera kwa mkwatibwi wokongolayo, Yesu. (Yohane 13:15, Aefeso 2-5, Chibvumbulutso 19-7) ngati mukuganiza za chithunzi cha malembo mmene moyo, wa, kristu umakomanilana—uli bwanji? yofunsilana—ndi madyelero a ukwati Mulungu atifunsa ife, ati, “ Ndili nacho chiyembekezo ine. Ngati ukhala ndi ine, yanganila kuti ndine yani, palibenso wina ofanana nane. Palibe padziko lapansi amene adzakwanilitse moyo wako monga: ine—chifukwa ndinakulenga wa ine. Zina ndi zonse ndi zochotsera iwe, koma ngati ungathe kulowera mbali yanga, udzaona mmene moyo umayenela, ndipo tidzakhala pa ukwati.” “ Konzeka Mkwatibwi”
4/8/2007